Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:3 Yeremiya, ptsa. 143-144
3 Yehova anabwera kwa ine kuchokera kutali, ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale.+ N’chifukwa chake ndakukoka mwa kukoma mtima kwanga kosatha.+