Yeremiya 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wanena kuti: “Fuulirani Yakobo mosangalala, fuulani kwambiri muli patsogolo pa mitundu ina ya anthu.+ Lengezani zimenezi.+ Tamandani Mulungu ndi kunena kuti, ‘Inu Yehova, pulumutsani anthu anu, otsalira a Isiraeli.’+
7 Yehova wanena kuti: “Fuulirani Yakobo mosangalala, fuulani kwambiri muli patsogolo pa mitundu ina ya anthu.+ Lengezani zimenezi.+ Tamandani Mulungu ndi kunena kuti, ‘Inu Yehova, pulumutsani anthu anu, otsalira a Isiraeli.’+