40 Chigwa chonse cha mitembo+ ndi cha phulusa+ losakanizika ndi mafuta, masitepe onse mpaka kukafika kuchigwa cha Kidironi,+ mpaka kukona ya Chipata cha Hatchi+ moyang’anana ndi kotulukira dzuwa, zidzakhala zoyera kwa Yehova.+ Mzindawu sudzazulidwa ndipo sudzapasulidwanso mpaka kalekale.”+