Yeremiya 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amene apatuka pa panganoli ndi akalonga a Yuda, akalonga a Yerusalemu,+ nduna za panyumba ya mfumu, ansembe ndi anthu onse a m’dzikoli amene anadutsa pakati pa mwana wa ng’ombe wodulidwa pakatiyo . . .
19 Amene apatuka pa panganoli ndi akalonga a Yuda, akalonga a Yerusalemu,+ nduna za panyumba ya mfumu, ansembe ndi anthu onse a m’dzikoli amene anadutsa pakati pa mwana wa ng’ombe wodulidwa pakatiyo . . .