Yeremiya 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika kumeneko Mikaya+ anawauza mawu onse amene anamva pamene Baruki anawerenga mokweza mumpukutu pamaso pa anthu onse.+
13 Atafika kumeneko Mikaya+ anawauza mawu onse amene anamva pamene Baruki anawerenga mokweza mumpukutu pamaso pa anthu onse.+