Yeremiya 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno akalongawo anamuuza kuti: “Khala pansi, ndipo uwerenge mokweza kuti timve.” Choncho Baruki+ anawawerengera mpukutuwo mokweza.
15 Ndiyeno akalongawo anamuuza kuti: “Khala pansi, ndipo uwerenge mokweza kuti timve.” Choncho Baruki+ anawawerengera mpukutuwo mokweza.