Yeremiya 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu itamva zimenezi inatuma Yehudi+ kuti akatenge mpukutuwo. Iye anakatenga mpukutuwo m’chipinda chodyera cha Elisama+ mlembi,+ moti Yehudiyo anayamba kuwerenga mokweza pamaso pa mfumu ndi akalonga onse amene anaimirira pafupi ndi mfumuyo.
21 Mfumu itamva zimenezi inatuma Yehudi+ kuti akatenge mpukutuwo. Iye anakatenga mpukutuwo m’chipinda chodyera cha Elisama+ mlembi,+ moti Yehudiyo anayamba kuwerenga mokweza pamaso pa mfumu ndi akalonga onse amene anaimirira pafupi ndi mfumuyo.