Yeremiya 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawiyi mfumu inali itakhala m’nyumba imene inali kukhala m’nyengo yozizira,+ ikuwotha moto wa mumbaula.+ Umenewu unali mwezi wa 9.*+
22 Pa nthawiyi mfumu inali itakhala m’nyumba imene inali kukhala m’nyengo yozizira,+ ikuwotha moto wa mumbaula.+ Umenewu unali mwezi wa 9.*+