Yeremiya 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yeremiya ananyamuka kuchoka ku Yerusalemu kupita kudziko la Benjamini+ kuti akalandire malo ake pakati pa anthu ake.
12 Yeremiya ananyamuka kuchoka ku Yerusalemu kupita kudziko la Benjamini+ kuti akalandire malo ake pakati pa anthu ake.