Yeremiya 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yeremiya anamuyankha kuti: “Zabodza zimenezo!+ Ine sindikuthawira kwa Akasidi.” Koma Iriya sanamumvere. Choncho iye anagwirabe Yeremiya ndi kumubweretsa kwa akalonga.
14 Yeremiya anamuyankha kuti: “Zabodza zimenezo!+ Ine sindikuthawira kwa Akasidi.” Koma Iriya sanamumvere. Choncho iye anagwirabe Yeremiya ndi kumubweretsa kwa akalonga.