Yeremiya 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yeremiya atalowa m’ndende ya pansiyo,+ m’kachipinda ka m’ndendemo, anakhala mmenemo kwa masiku ambiri.
16 Yeremiya atalowa m’ndende ya pansiyo,+ m’kachipinda ka m’ndendemo, anakhala mmenemo kwa masiku ambiri.