Yeremiya 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Yeremiya anafunsa Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthu onse,+ kuti munditsekere m’ndende?
18 Pamenepo Yeremiya anafunsa Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthu onse,+ kuti munditsekere m’ndende?