Yeremiya 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu maso a Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga m’maunyolo amkuwa kuti apite naye ku Babulo.
7 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu maso a Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga m’maunyolo amkuwa kuti apite naye ku Babulo.