Yeremiya 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno ena mwa anthuwo, anthu onyozeka amene analibe kalikonse, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya m’dziko la Yuda,+ ndipo pa tsiku limenelo anawapatsa minda ya mpesa ndi ntchito zokakamiza kuti azigwira.+
10 Ndiyeno ena mwa anthuwo, anthu onyozeka amene analibe kalikonse, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya m’dziko la Yuda,+ ndipo pa tsiku limenelo anawapatsa minda ya mpesa ndi ntchito zokakamiza kuti azigwira.+