-
Yeremiya 39:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kuwonjezera pamenepo, Nebukadirezara mfumu ya Babulo anapereka lamulo lokhudza Yeremiya kwa Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, kuti:
-