Yeremiya 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.
14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.