-
Yeremiya 41:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chitsime chimene Isimaeli+ anaponyamo mitembo yonse ya amuna amene anawapha chinali chachikulu kwambiri. Mfumu Asa ndi imene inakumba chitsime chimenechi pamene Basa mfumu ya Isiraeli inamuopseza.+ Chitsime chimenechi ndi chimene Isimaeli mwana wa Netaniya anaponyamo mitembo ya anthu amene anawapha.
-