Yeremiya 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yeremiya anapitiriza kuuza anthu onse ndi akazi onse kuti: “Tamverani mawu a Yehova inu nonse a ku Yuda amene muli ku Iguputo kuno.+
24 Ndiyeno Yeremiya anapitiriza kuuza anthu onse ndi akazi onse kuti: “Tamverani mawu a Yehova inu nonse a ku Yuda amene muli ku Iguputo kuno.+