Yeremiya 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga, ndikuzigwetsa, ndipo zimene ndabzala, ndikuzizula. Ndichita zimenezi m’dziko lonse.+
4 “Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga, ndikuzigwetsa, ndipo zimene ndabzala, ndikuzizula. Ndichita zimenezi m’dziko lonse.+