Yeremiya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu asilikali okwera pamahatchi, mangani mahatchi anu ndi kukwerapo, ndipo muvale zisoti zanu ndi kukhala okonzeka. Pukutani mikondo yanu ing’onoing’ono. Valani zovala zanu zamamba achitsulo.+
4 Inu asilikali okwera pamahatchi, mangani mahatchi anu ndi kukwerapo, ndipo muvale zisoti zanu ndi kukhala okonzeka. Pukutani mikondo yanu ing’onoing’ono. Valani zovala zanu zamamba achitsulo.+