Yeremiya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Iwe namwali, mwana wamkazi wa Iguputo,+ pita ku Giliyadi kuti ukatenge mafuta a basamu.+ Wachulukitsa njira zochiritsira zosathandiza koma sudzachiritsidwa.+
11 “Iwe namwali, mwana wamkazi wa Iguputo,+ pita ku Giliyadi kuti ukatenge mafuta a basamu.+ Wachulukitsa njira zochiritsira zosathandiza koma sudzachiritsidwa.+