Yeremiya 46:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndilanga Amoni+ wa ku No,+ Farao, Iguputo pamodzi ndi milungu yake+ ndi mafumu ake.+ Ndilanga Farao ndi onse amene amamukhulupirira.’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:25 Nsanja ya Olonda,7/1/2003, tsa. 32
25 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndilanga Amoni+ wa ku No,+ Farao, Iguputo pamodzi ndi milungu yake+ ndi mafumu ake.+ Ndilanga Farao ndi onse amene amamukhulupirira.’+