Yeremiya 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+
3 Abambo adzathawa osayang’ana m’mbuyo kuti apulumutse ana awo. Adzachita izi chifukwa chakuti sadzalimba mtima pakumva mgugu wa mahatchi ake,+ phokoso la magaleta ake ankhondo+ ndi kulira kwa mawilo ake.+