Yeremiya 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kodi lupangali lingakhale chete bwanji pamene Yehova ndi amene walilamula? Liyenera kupita ku Asikeloni ndi m’mphepete mwa nyanja.+ Iye walituma kuti likakhale kumeneko.”
7 “Kodi lupangali lingakhale chete bwanji pamene Yehova ndi amene walilamula? Liyenera kupita ku Asikeloni ndi m’mphepete mwa nyanja.+ Iye walituma kuti likakhale kumeneko.”