Yeremiya 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu akupita ku Luhiti+ akulira. Akupita akulira kwambiri. Amene akutsika kuchokera ku Horonaimu akufuula mowawidwa mtima chifukwa amva za chiwonongeko.+
5 Anthu akupita ku Luhiti+ akulira. Akupita akulira kwambiri. Amene akutsika kuchokera ku Horonaimu akufuula mowawidwa mtima chifukwa amva za chiwonongeko.+