Yeremiya 48:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Anthu inu perekani chizindikiro cha pamsewu kwa anthu a ku Mowabu pakuti adzachoka pamene dziko lawo likusanduka bwinja.+ Mizinda yake idzasanduka chinthu chodabwitsa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo.+
9 “Anthu inu perekani chizindikiro cha pamsewu kwa anthu a ku Mowabu pakuti adzachoka pamene dziko lawo likusanduka bwinja.+ Mizinda yake idzasanduka chinthu chodabwitsa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo.+