Yeremiya 48:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Nyanga* ya Mowabu yadulidwa+ ndipo dzanja lake lathyoledwa,’+ watero Yehova.