Yeremiya 48:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Ine ndadziwa za mkwiyo wake,’ watero Yehova, ‘ndipo kudzikuza kwakeko sikudzaphula kanthu.+ Iye sadzachita zonena zake zopanda pakezo.+
30 “‘Ine ndadziwa za mkwiyo wake,’ watero Yehova, ‘ndipo kudzikuza kwakeko sikudzaphula kanthu.+ Iye sadzachita zonena zake zopanda pakezo.+