Yeremiya 48:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndidzachititsa kuti m’dziko la Mowabu musapezeke aliyense wobweretsa nsembe kumalo okwezeka komanso wofukiza nsembe yautsi kwa mulungu wake,’+ watero Yehova.
35 Ndidzachititsa kuti m’dziko la Mowabu musapezeke aliyense wobweretsa nsembe kumalo okwezeka komanso wofukiza nsembe yautsi kwa mulungu wake,’+ watero Yehova.