Yeremiya 49:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Aelamu ndidzawachititsa mantha pamaso pa adani awo ndi pamaso pa anthu amene akufunafuna moyo wawo. Ndidzawabweretsera tsoka, mkwiyo wanga woyaka moto,”+ watero Yehova. “Ndidzawatumizira lupanga kufikira nditawafafaniza.”+
37 “Aelamu ndidzawachititsa mantha pamaso pa adani awo ndi pamaso pa anthu amene akufunafuna moyo wawo. Ndidzawabweretsera tsoka, mkwiyo wanga woyaka moto,”+ watero Yehova. “Ndidzawatumizira lupanga kufikira nditawafafaniza.”+