Yeremiya 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mayi wa anthu inu wachita manyazi kwambiri.+ Mayi amene anakuberekani wakhumudwa kwambiri.+ Taonani! Iye ndi wosafunika kwenikweni pakati pa mitundu ina, wakhala ngati dera lopanda madzi ndiponso chipululu.+
12 Mayi wa anthu inu wachita manyazi kwambiri.+ Mayi amene anakuberekani wakhumudwa kwambiri.+ Taonani! Iye ndi wosafunika kwenikweni pakati pa mitundu ina, wakhala ngati dera lopanda madzi ndiponso chipululu.+