Yeremiya 50:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Lowani m’dziko lake kuchokera kudera lakutali.+ Tsegulani nkhokwe zake.+ Muunjikeni pamodzi ngati mmene anthu amaunjikira milu ya tirigu+ ndipo mumuwonongeretu.+ M’dzikomo musapezeke aliyense wotsala.+
26 Lowani m’dziko lake kuchokera kudera lakutali.+ Tsegulani nkhokwe zake.+ Muunjikeni pamodzi ngati mmene anthu amaunjikira milu ya tirigu+ ndipo mumuwonongeretu.+ M’dzikomo musapezeke aliyense wotsala.+