Yeremiya 50:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pa tsiku limenelo Babulo Wodzikuza ameneyu adzapunthwa ndi kugwa+ ndipo sipadzapezeka wina womudzutsa.+ Mizinda imene iye amalamulira ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzawononganso madera onse ozungulira mizindayo.”+
32 Pa tsiku limenelo Babulo Wodzikuza ameneyu adzapunthwa ndi kugwa+ ndipo sipadzapezeka wina womudzutsa.+ Mizinda imene iye amalamulira ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzawononganso madera onse ozungulira mizindayo.”+