Maliro 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira+ mawu a pakamwa pake.Anthu nonsenu, tamverani mawu anga, ndipo muone ululu umene ndikumva.Anamwali anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
18 Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndapandukira+ mawu a pakamwa pake.Anthu nonsenu, tamverani mawu anga, ndipo muone ululu umene ndikumva.Anamwali anga ndi anyamata anga atengedwa kupita ku ukapolo.+