Maliro 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wafooketsa thupi langa ndipo wachititsa khungu langa kunyala.+ Iye waphwanyanso mafupa anga.+