Maliro 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso ndikalira ndi kupempha thandizo mofuula, iye amatsekereza pemphero+ langa.