Maliro 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu mwanditayira kutali, moti sindilinso pa mtendere. Sindikukumbukiranso zinthu zabwino.+