Ezekieli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapiko a chamoyo china anali kukhudzana ndi a chamoyo china. Zamoyozo sizinali kutembenuka zikamayenda. Chilichonse chinkangopita kutsogolo basi.+
9 Mapiko a chamoyo china anali kukhudzana ndi a chamoyo china. Zamoyozo sizinali kutembenuka zikamayenda. Chilichonse chinkangopita kutsogolo basi.+