Ezekieli 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amuna inu, simudzapita kukakhala m’mipata ya mpanda+ kuti mukamenye nkhondo, kapena kuti mukamangire nyumba ya Isiraeli mpanda wamiyala+ n’cholinga chakuti mudzadziteteze pa nkhondo ya m’tsiku la Yehova.”+
5 Amuna inu, simudzapita kukakhala m’mipata ya mpanda+ kuti mukamenye nkhondo, kapena kuti mukamangire nyumba ya Isiraeli mpanda wamiyala+ n’cholinga chakuti mudzadziteteze pa nkhondo ya m’tsiku la Yehova.”+