Ezekieli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+