Ezekieli 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Mkwiyo wanga ndidzauthetsera pakhomalo ndiponso pa anthu amene analipaka laimu. Anthu inu ndidzakuuzani kuti: “Khoma lija kulibe, komanso anthu amene analipaka laimu aja kulibe,+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:15 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
15 “‘Mkwiyo wanga ndidzauthetsera pakhomalo ndiponso pa anthu amene analipaka laimu. Anthu inu ndidzakuuzani kuti: “Khoma lija kulibe, komanso anthu amene analipaka laimu aja kulibe,+