Ezekieli 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma iwe mwana wa munthu, yang’ana+ kwa ana aakazi a anthu a mtundu wako, amene akulosera+ zam’mutu mwawo+ monga aneneri aakazi, ndipo ulosere zoipa zimene zidzawachitikire.
17 “Koma iwe mwana wa munthu, yang’ana+ kwa ana aakazi a anthu a mtundu wako, amene akulosera+ zam’mutu mwawo+ monga aneneri aakazi, ndipo ulosere zoipa zimene zidzawachitikire.