Ezekieli 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nding’amba zovala zanu zakumutu ndi kulanditsa anthu anga m’manja mwanu, ndipo iwo sadzakhalanso m’manja mwanu ngati zinthu zogwidwa posaka. Chotero inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
21 Nding’amba zovala zanu zakumutu ndi kulanditsa anthu anga m’manja mwanu, ndipo iwo sadzakhalanso m’manja mwanu ngati zinthu zogwidwa posaka. Chotero inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+