Ezekieli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa chakuti mwakhumudwitsa mtima wa munthu wolungama mwa chinyengo chanu,+ pamene ineyo sindinamukhumudwitse, ndiponso chifukwa chakuti mwalimbitsa manja a munthu woipa+ kuti asasiye njira zake zoipa, n’kukhala ndi moyo,+
22 Chifukwa chakuti mwakhumudwitsa mtima wa munthu wolungama mwa chinyengo chanu,+ pamene ineyo sindinamukhumudwitse, ndiponso chifukwa chakuti mwalimbitsa manja a munthu woipa+ kuti asasiye njira zake zoipa, n’kukhala ndi moyo,+