-
Ezekieli 14:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pakuti munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo amene akukhala mu Isiraeli, amene wasiya kunditsatira+ n’kuika mtima wake pamafano ake onyansa, ndiponso amene waika pamaso pake chinthu chopunthwitsa chimene chimamulakwitsa n’kupita kwa mneneri kuti akafunsire kwa ine,+ ine Yehova ndidzamuyankha ndekha.
-