16 ngakhale zikanakhala kuti amuna atatu amenewa anali kukhala m’dzikolo, pali ine Mulungu wamoyo, iwo sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena aakazi. Iwo okhawo ndiwo akanapulumutsidwa, koma dzikolo likanakhala bwinja lokhalokha,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”