Ezekieli 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ngakhale amuna atatu amenewa akanakhalamo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena ana awo aakazi, koma iwo okhawo ndiwo akanapulumutsidwa,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
18 ngakhale amuna atatu amenewa akanakhalamo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena ana awo aakazi, koma iwo okhawo ndiwo akanapulumutsidwa,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”