Ezekieli 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Ndithu iwo adzakutonthozani mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo. Chotero mudzadziwa kuti zonse zimene ndidzachitire mzindawo, sindinazichite popanda chifukwa,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+
23 “‘Ndithu iwo adzakutonthozani mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo. Chotero mudzadziwa kuti zonse zimene ndidzachitire mzindawo, sindinazichite popanda chifukwa,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+