Ezekieli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+
15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+