Ezekieli 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘“Maso anga anayamba kuwamvera chisoni kuti ndisawawononge,+ chotero sindinawafafanize m’chipululu.
17 “‘“Maso anga anayamba kuwamvera chisoni kuti ndisawawononge,+ chotero sindinawafafanize m’chipululu.